Yesaya 66:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Popeza ndikudziwa ntchito zawo+ ndi maganizo awo,+ ine ndikubwera kudzasonkhanitsa pamodzi mitundu yonse ndi zilankhulo zonse za anthu,+ ndipo iwo adzabwera n’kuona ulemerero wanga.”+
18 “Popeza ndikudziwa ntchito zawo+ ndi maganizo awo,+ ine ndikubwera kudzasonkhanitsa pamodzi mitundu yonse ndi zilankhulo zonse za anthu,+ ndipo iwo adzabwera n’kuona ulemerero wanga.”+