Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 37:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ukakhala phee, ukamatuluka,+ ndiponso ukamalowa, ine ndimadziwa bwino,+

      Ndimadziwanso ukandipsera mtima,+

  • Yesaya 59:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ukonde wawo wa kangaude sudzakhala chovala chawo, ndipo iwo sadzavala zochita zawo.+ Ntchito zawo n’zopweteka ena, ndipo m’manja mwawo muli ntchito zachiwawa.+

  • Amosi 5:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pakuti ndadziwa kuchuluka kwa zochita zanu zondipandukira+ ndiponso kukula kwa machimo anu,+ inu amene mukuchitira nkhanza munthu wolungama,+ amene mukulandira ndalama za chitsekapakamwa+ ndiponso amene mukupondereza anthu osauka+ pachipata cha mzinda.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena