-
Yeremiya 29:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Zimenezi zidzawachitikira chifukwa chakuti akhala akuchita zinthu zopanda nzeru mu Isiraeli,+ ndipo akupitiriza kuchita chigololo ndi akazi a anzawo.+ Komanso akupitiriza kulankhula zonama m’dzina langa. Iwo akulankhula mawu amene sindinawalamule kuti akanene.+
“‘“Ine ndikuzidziwa zimenezi ndipo ndine mboni yake,”+ watero Yehova.’”
-