Deuteronomo 28:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Yehova adzakulitsa kwambiri miliri yako ndi miliri ya ana ako. Miliri imeneyo idzakhala yaikulu kwambiri ndi yokhalitsa,+ ndipo udzagwidwa ndi matenda onyansa ndi okhalitsa.+ Deuteronomo 29:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Pamenepo m’badwo wa m’tsogolo, ana anu amene adzabwera pambuyo panu, ndiponso mlendo amene adzachokera kudziko lakutali, akadzaona miliri ndi nthenda zimene Yehova wakantha nazo dzikolo,+ adzanena mawu.
59 Yehova adzakulitsa kwambiri miliri yako ndi miliri ya ana ako. Miliri imeneyo idzakhala yaikulu kwambiri ndi yokhalitsa,+ ndipo udzagwidwa ndi matenda onyansa ndi okhalitsa.+
22 “Pamenepo m’badwo wa m’tsogolo, ana anu amene adzabwera pambuyo panu, ndiponso mlendo amene adzachokera kudziko lakutali, akadzaona miliri ndi nthenda zimene Yehova wakantha nazo dzikolo,+ adzanena mawu.