Deuteronomo 28:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova adzakulanga ndi chifuwa chachikulu,+ kuphwanya kwa thupi koopsa, kutupa, kutentha thupi kwambiri, lupanga,+ mphepo yotentha yowononga mbewu+ ndi matenda a mbewu.+ Zimenezi zidzakusautsa kufikira utawonongeka. 2 Mbiri 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iweyo udzakhala wodwaladwala+ popeza udzadwala matenda a m’matumbo, mpaka matumbo ako adzatuluka chifukwa chodwala tsiku ndi tsiku.’”+
22 Yehova adzakulanga ndi chifuwa chachikulu,+ kuphwanya kwa thupi koopsa, kutupa, kutentha thupi kwambiri, lupanga,+ mphepo yotentha yowononga mbewu+ ndi matenda a mbewu.+ Zimenezi zidzakusautsa kufikira utawonongeka.
15 Iweyo udzakhala wodwaladwala+ popeza udzadwala matenda a m’matumbo, mpaka matumbo ako adzatuluka chifukwa chodwala tsiku ndi tsiku.’”+