Yeremiya 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Monga mmene chitsime chimasungira madzi ake ali ozizira, Yerusalemu wasunga zoipa zake ngati zinthu zabwino. Mkati mwake mumamveka zachiwawa ndi kufunkha.+ Nthawi zonse ndimaona matenda ndi miliri mumzindawo. Amosi 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthuwo sadziwa kuchita zolungama,+ ndipo asonkhanitsa munsanja zawo zokhalamo zinthu zimene anafunkha mwachiwawa,”+ watero Yehova.’ Mika 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu olemera a mumzindawo amakonda kuchita zachiwawa. Anthu okhalamo akulankhula zonama+ ndipo lilime la m’kamwa mwawo ndi lachinyengo.+
7 Monga mmene chitsime chimasungira madzi ake ali ozizira, Yerusalemu wasunga zoipa zake ngati zinthu zabwino. Mkati mwake mumamveka zachiwawa ndi kufunkha.+ Nthawi zonse ndimaona matenda ndi miliri mumzindawo.
10 Anthuwo sadziwa kuchita zolungama,+ ndipo asonkhanitsa munsanja zawo zokhalamo zinthu zimene anafunkha mwachiwawa,”+ watero Yehova.’
12 Anthu olemera a mumzindawo amakonda kuchita zachiwawa. Anthu okhalamo akulankhula zonama+ ndipo lilime la m’kamwa mwawo ndi lachinyengo.+