Miyambo 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ukapitiriza kugona pang’ono, ukapitiriza katulo pang’ono, ukapitiriza kupinda manja pang’ono pogona,+ Maliko 13:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 kuti akadzafika mwadzidzidzi, asadzakupezeni mukugona.+
10 Ukapitiriza kugona pang’ono, ukapitiriza katulo pang’ono, ukapitiriza kupinda manja pang’ono pogona,+