2 Mafumu 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawi imeneyo Rezini+ mfumu ya Siriya ndi Peka+ mwana wa Remaliya mfumu ya Isiraeli, anabwera kudzaukira Yerusalemu mwankhondo ndipo anazungulira Ahazi koma sanathe kumenyana naye.+
5 Pa nthawi imeneyo Rezini+ mfumu ya Siriya ndi Peka+ mwana wa Remaliya mfumu ya Isiraeli, anabwera kudzaukira Yerusalemu mwankhondo ndipo anazungulira Ahazi koma sanathe kumenyana naye.+