2 Mbiri 28:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho Yehova Mulungu wake anam’pereka m’manja+ mwa mfumu ya Siriya+ moti Asiriya anam’gonjetsa n’kugwira anthu ake ambiri kupita nawo ku Damasiko.+ Anam’perekanso m’manja mwa mfumu ya Isiraeli+ ndipo inam’gonjetsa n’kupha anthu ake ambirimbiri.
5 Choncho Yehova Mulungu wake anam’pereka m’manja+ mwa mfumu ya Siriya+ moti Asiriya anam’gonjetsa n’kugwira anthu ake ambiri kupita nawo ku Damasiko.+ Anam’perekanso m’manja mwa mfumu ya Isiraeli+ ndipo inam’gonjetsa n’kupha anthu ake ambirimbiri.