Yobu 29:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndinkavala chilungamo, ndipo icho chinkandiveka.+Chilungamo changa chinali ngati malaya akunja odula manja, ndi nduwira.* Yesaya 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chilungamo ndi kukhulupirika zidzakhala lamba wa m’chiuno mwake.+
14 Ndinkavala chilungamo, ndipo icho chinkandiveka.+Chilungamo changa chinali ngati malaya akunja odula manja, ndi nduwira.*