Aefeso 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Komanso landirani chisoti cholimba+ chachipulumutso, ndiponso lupanga+ la mzimu,+ lomwe ndilo mawu a Mulungu.+ 1 Atesalonika 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma ife amene tili a usana, tikhalebe oganiza bwino ndipo tivale chodzitetezera pachifuwa+ chachikhulupiriro+ ndi chikondi. Tivalenso chiyembekezo chachipulumutso+ monga chisoti,+
17 Komanso landirani chisoti cholimba+ chachipulumutso, ndiponso lupanga+ la mzimu,+ lomwe ndilo mawu a Mulungu.+
8 Koma ife amene tili a usana, tikhalebe oganiza bwino ndipo tivale chodzitetezera pachifuwa+ chachikhulupiriro+ ndi chikondi. Tivalenso chiyembekezo chachipulumutso+ monga chisoti,+