1 Mafumu 11:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ndidzachititsa manyazi ana a Davide chifukwa cha zoipa zimene anachita,+ koma osati nthawi zonse.’”+ Yesaya 54:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Kwa kanthawi kochepa ndinakusiyiratu,+ koma ndidzakusonkhanitsa pamodzi mwachifundo chachikulu.+
39 Ndidzachititsa manyazi ana a Davide chifukwa cha zoipa zimene anachita,+ koma osati nthawi zonse.’”+