2 Mafumu 9:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndiyeno Yehu anati: “M’ponyeni+ pansi Yezebeliyo!” Iwo anam’ponyadi pansi, ndipo magazi ake ena anamwazika n’kuwaza khoma ndi mahatchi. Kenako Yehu anam’pondaponda+ ndi mahatchi ake.
33 Ndiyeno Yehu anati: “M’ponyeni+ pansi Yezebeliyo!” Iwo anam’ponyadi pansi, ndipo magazi ake ena anamwazika n’kuwaza khoma ndi mahatchi. Kenako Yehu anam’pondaponda+ ndi mahatchi ake.