Genesis 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ana a Yavani anali Elisaha,+ Tarisi,+ Kitimu+ ndi Dodanimu.+ Salimo 72:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mafumu a ku Tarisi ndi m’zilumba+Adzapereka msonkho.+Mafumu a ku Sheba ndi SebaAdzapereka mphatso.+
10 Mafumu a ku Tarisi ndi m’zilumba+Adzapereka msonkho.+Mafumu a ku Sheba ndi SebaAdzapereka mphatso.+