1 Mbiri 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Davide anapha Hadadezeri+ mfumu ya Zoba+ ku Hamati,+ pamene Hadadezeriyo anali kupita kumtsinje wa Firate+ kukakhazikitsa ulamuliro wake kumeneko. Yesaya 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “M’tsiku limenelo, pogwiritsira ntchito lezala lobwereka la kuchigawo cha ku Mtsinje,*+ pogwiritsira ntchito mfumu ya Asuri,+ Yehova adzameta tsitsi la kumutu ndi tsitsi la m’mapazi, ndipo lezalalo lidzachotseratu ngakhale ndevu.+
3 Davide anapha Hadadezeri+ mfumu ya Zoba+ ku Hamati,+ pamene Hadadezeriyo anali kupita kumtsinje wa Firate+ kukakhazikitsa ulamuliro wake kumeneko.
20 “M’tsiku limenelo, pogwiritsira ntchito lezala lobwereka la kuchigawo cha ku Mtsinje,*+ pogwiritsira ntchito mfumu ya Asuri,+ Yehova adzameta tsitsi la kumutu ndi tsitsi la m’mapazi, ndipo lezalalo lidzachotseratu ngakhale ndevu.+