Yobu 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zoipa zimene munthu anachita, Mulungu adzazisungira ana ake omwe,+Adzam’patsa mphoto yake, ndipo iye adzaidziwa.+ Ezekieli 33:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma mawu ako akadzakwaniritsidwa, pakuti adzakwaniritsidwa ndithu,+ iwo adzadziwa kuti pakati pawo panalidi mneneri.”+
19 Zoipa zimene munthu anachita, Mulungu adzazisungira ana ake omwe,+Adzam’patsa mphoto yake, ndipo iye adzaidziwa.+
33 Koma mawu ako akadzakwaniritsidwa, pakuti adzakwaniritsidwa ndithu,+ iwo adzadziwa kuti pakati pawo panalidi mneneri.”+