Deuteronomo 32:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Vinyo wawo ndi poizoni wa njoka zikuluzikulu,Ndiponso ndi poizoni wakupha wa mamba.+ Salimo 58:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo ali ndi poizoni ngati wa njoka,+Ndipo ndi ogontha ngati njoka ya mamba imene yatseka makutu ake,+
4 Iwo ali ndi poizoni ngati wa njoka,+Ndipo ndi ogontha ngati njoka ya mamba imene yatseka makutu ake,+