Salimo 58:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo ali ndi poizoni ngati wa njoka,+Ndipo ndi ogontha ngati njoka ya mamba imene yatseka makutu ake,+ Salimo 140:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anola lilime lawo ndipo lakhala ngati la njoka.+M’milomo yawo muli poizoni wa mphiri.+ [Seʹlah.]
4 Iwo ali ndi poizoni ngati wa njoka,+Ndipo ndi ogontha ngati njoka ya mamba imene yatseka makutu ake,+ Salimo 140:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anola lilime lawo ndipo lakhala ngati la njoka.+M’milomo yawo muli poizoni wa mphiri.+ [Seʹlah.]