Salimo 47:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Imbani nyimbo zotamanda Mulungu, imbani nyimbo zotamanda.+Imbani nyimbo zotamanda Mfumu yathu, imbani nyimbo zotamanda. Salimo 149:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atamande dzina lake mwa kuvina.+Amuimbire nyimbo zomutamanda ndi maseche ndi zeze,+
6 Imbani nyimbo zotamanda Mulungu, imbani nyimbo zotamanda.+Imbani nyimbo zotamanda Mfumu yathu, imbani nyimbo zotamanda.