Salimo 81:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yambani kuimba nyimbo+ ndipo tengani maseche,+Zeze womveka mosangalatsa pamodzi ndi choimbira cha zingwe.+ Salimo 144:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu Mulungu, ine ndidzakuimbirani nyimbo yatsopano.+Ndidzaimba nyimbo yokutamandani ndi choimbira cha zingwe 10.+ Salimo 150:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mutamandeni ndi maseche+ ndi gule wovina mozungulira.+Mutamandeni ndi zoimbira za zingwe+ ndi chitoliro.+
2 Yambani kuimba nyimbo+ ndipo tengani maseche,+Zeze womveka mosangalatsa pamodzi ndi choimbira cha zingwe.+
9 Inu Mulungu, ine ndidzakuimbirani nyimbo yatsopano.+Ndidzaimba nyimbo yokutamandani ndi choimbira cha zingwe 10.+ Salimo 150:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mutamandeni ndi maseche+ ndi gule wovina mozungulira.+Mutamandeni ndi zoimbira za zingwe+ ndi chitoliro.+
4 Mutamandeni ndi maseche+ ndi gule wovina mozungulira.+Mutamandeni ndi zoimbira za zingwe+ ndi chitoliro.+