Habakuku 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ine ndikuutsa Akasidi,+ mtundu waukali ndi waphuma umene ukupita kumalo otakasuka a padziko lapansi kukatenga malo amene si awo.+ Zekariya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndakwiyira kwambiri anthu a mitundu ina amene akukhala mwabata.+ Ndawakwiyira chifukwa chakuti ine ndinangokwiyira anthu anga pang’ono pokha,+ koma anthu amenewa anakulitsa tsoka la anthu angawo.”’+
6 Ine ndikuutsa Akasidi,+ mtundu waukali ndi waphuma umene ukupita kumalo otakasuka a padziko lapansi kukatenga malo amene si awo.+
15 Ndakwiyira kwambiri anthu a mitundu ina amene akukhala mwabata.+ Ndawakwiyira chifukwa chakuti ine ndinangokwiyira anthu anga pang’ono pokha,+ koma anthu amenewa anakulitsa tsoka la anthu angawo.”’+