Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 “Yehova adzautsa mtundu wakutali, kumalekezero a dziko,+ mtundu umene chilankhulo chake sudzachimva.+ Mtunduwo udzakuukira monga mmene chiwombankhanga chimakhwathulira nyama yake,+

  • Yeremiya 5:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Tsopano anthu inu, ndikukubweretserani mtundu wa anthu akutali,+ inu a m’nyumba ya Isiraeli,” watero Yehova. “Umenewu ndi mtundu umene wakhalapo kwa nthawi yaitali,+ mtundu wakale, mtundu umene chilankhulo chawo simuchidziwa ndipo simungamve ndi kuzindikira zimene akulankhula.

  • Yeremiya 6:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Yehova wanena kuti: “Taonani! Anthu akubwera kuchokera kudziko la kumpoto. Pali mtundu wamphamvu umene udzadzutsidwa kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+

  • Ezekieli 23:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndidzabweretsa ana aamuna a ku Babulo,+ Akasidi onse,+ amuna a ku Pekodi,+ a ku Sowa, a ku Kowa, pamodzi ndi ana aamuna a ku Asuri. Onsewa ndiwo anyamata osiririka, abwanamkubwa, atsogoleri, amuna ankhondo, amuna ochita kusankhidwa ndi okwera pamahatchi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena