2 Mafumu 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pambuyo pake mneneri Yesaya anapita kwa Mfumu Hezekiya n’kuifunsa kuti:+ “Kodi anthu aja anena kuti chiyani, ndipo anachokera kuti?”+ Hezekiya anayankha kuti: “Anachokera kudziko lakutali, ku Babulo.” Yesaya 39:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pambuyo pake, mneneri Yesaya anapita kwa Mfumu Hezekiya n’kuifunsa kuti:+ “Kodi anthu aja anena kuti chiyani, ndipo anachokera kuti?” Hezekiya anayankha kuti: “Anachokera kudziko lakutali, ku Babulo.”+ Ezekieli 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Koma iwe mwana wa munthu, konza misewu iwiri yoti lupanga la mfumu ya Babulo lidzadutsemo.+ Misewu yonseyo ichokere m’dziko limodzi. Pamsewu wopita mumzindawo, uikepo chikwangwani cholozera kumeneko.+
14 Pambuyo pake mneneri Yesaya anapita kwa Mfumu Hezekiya n’kuifunsa kuti:+ “Kodi anthu aja anena kuti chiyani, ndipo anachokera kuti?”+ Hezekiya anayankha kuti: “Anachokera kudziko lakutali, ku Babulo.”
3 Pambuyo pake, mneneri Yesaya anapita kwa Mfumu Hezekiya n’kuifunsa kuti:+ “Kodi anthu aja anena kuti chiyani, ndipo anachokera kuti?” Hezekiya anayankha kuti: “Anachokera kudziko lakutali, ku Babulo.”+
19 “Koma iwe mwana wa munthu, konza misewu iwiri yoti lupanga la mfumu ya Babulo lidzadutsemo.+ Misewu yonseyo ichokere m’dziko limodzi. Pamsewu wopita mumzindawo, uikepo chikwangwani cholozera kumeneko.+