Ezekieli 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Iwe mwana wa munthu, tenga njerwa ndipo uiike pamaso pako. Panjerwapo ujambulepo mzinda wa Yerusalemu.+ Ezekieli 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Iwe mwana wa munthu, tenga lupanga lakuthwa. Likhale ngati lezala lako lometela ndipo umetele tsitsi lako ndi ndevu zako.+ Kenako utenge sikelo yoyezera ndipo ugawe tsitsilo m’magawo atatu.
4 “Iwe mwana wa munthu, tenga njerwa ndipo uiike pamaso pako. Panjerwapo ujambulepo mzinda wa Yerusalemu.+
5 “Iwe mwana wa munthu, tenga lupanga lakuthwa. Likhale ngati lezala lako lometela ndipo umetele tsitsi lako ndi ndevu zako.+ Kenako utenge sikelo yoyezera ndipo ugawe tsitsilo m’magawo atatu.