Levitiko 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Asamete mpala mitu yawo,+ asamete ndevu za m’masaya mwawo+ ndipo asadzitemeteme thupi lawo.+ Ezekieli 44:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Asamamete tsitsi la kumutu kwawo,+ komanso tsitsilo lisamatalike kwambiri, chotero tsitsilo azilidulira.+
20 Asamamete tsitsi la kumutu kwawo,+ komanso tsitsilo lisamatalike kwambiri, chotero tsitsilo azilidulira.+