2 Mafumu 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano Yehova anayamba kum’tumizira Yehoyakimu magulu a achifwamba a Akasidi,+ a Asiriya, a Amowabu,+ ndi a ana a Amoni. Ankawatumiza ku Yuda kuti awononge dzikolo mogwirizana ndi mawu a Yehova+ amene analankhula kudzera mwa atumiki ake, aneneri. Yesaya 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Taonani dziko la Akasidi.+ Anthu awa, osati Asuri,+ ndi amene anapanga mzindawo kuti ukhale malo okhala nyama zam’chipululu.+ Amanga nsanja zawo zomenyerapo nkhondo.+ Agumula nyumba zake zachifumu.+ Iwo asandutsa mzindawo bwinja logumukagumuka.+
2 Tsopano Yehova anayamba kum’tumizira Yehoyakimu magulu a achifwamba a Akasidi,+ a Asiriya, a Amowabu,+ ndi a ana a Amoni. Ankawatumiza ku Yuda kuti awononge dzikolo mogwirizana ndi mawu a Yehova+ amene analankhula kudzera mwa atumiki ake, aneneri.
13 Taonani dziko la Akasidi.+ Anthu awa, osati Asuri,+ ndi amene anapanga mzindawo kuti ukhale malo okhala nyama zam’chipululu.+ Amanga nsanja zawo zomenyerapo nkhondo.+ Agumula nyumba zake zachifumu.+ Iwo asandutsa mzindawo bwinja logumukagumuka.+