Yesaya 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Taonani dziko la Akasidi.+ Anthu awa, osati Asuri,+Ndi amene anapanga mzindawo kuti ukhale malo okhala nyama zamʼchipululu. Amanga nsanja zawo zomenyerapo nkhondo.Agumula nyumba zake zachifumu zokhala ndi mpanda wolimba,+Ndipo iwo asandutsa mzindawo kukhala bwinja lokhalokha. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:13 Yesaya 1, ptsa. 252-253
13 Taonani dziko la Akasidi.+ Anthu awa, osati Asuri,+Ndi amene anapanga mzindawo kuti ukhale malo okhala nyama zamʼchipululu. Amanga nsanja zawo zomenyerapo nkhondo.Agumula nyumba zake zachifumu zokhala ndi mpanda wolimba,+Ndipo iwo asandutsa mzindawo kukhala bwinja lokhalokha.