Yesaya 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Taonani dziko la Akasidi.+ Anthu awa, osati Asuri,+ ndi amene anapanga mzindawo kuti ukhale malo okhala nyama zam’chipululu.+ Amanga nsanja zawo zomenyerapo nkhondo.+ Agumula nyumba zake zachifumu.+ Iwo asandutsa mzindawo bwinja logumukagumuka.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:13 Yesaya 1, ptsa. 252-253
13 Taonani dziko la Akasidi.+ Anthu awa, osati Asuri,+ ndi amene anapanga mzindawo kuti ukhale malo okhala nyama zam’chipululu.+ Amanga nsanja zawo zomenyerapo nkhondo.+ Agumula nyumba zake zachifumu.+ Iwo asandutsa mzindawo bwinja logumukagumuka.+