Yesaya 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova akadzamaliza ntchito yake yonse mʼphiri la Ziyoni komanso mu Yerusalemu, adzalanga mfumu ya Asuri chifukwa cha mwano umene uli mumtima mwake ndiponso chifukwa chakuti amayangʼana monyada ndi modzikuza.+ Nahumu 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Abusa ako ayamba kuodzera, iwe mfumu ya Asuri,Ndipo anthu ako olemekezeka akungokhala mʼnyumba zawo. Anthu ako amwazikana mʼmapiri,Ndipo palibe amene akuwasonkhanitsa.+ Zefaniya 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye adzaloza dzanja lake kumpoto ndipo adzawononga Asuri.Adzachititsa Nineve kukhala bwinja,+ kukhala dziko louma ngati chipululu.
12 Yehova akadzamaliza ntchito yake yonse mʼphiri la Ziyoni komanso mu Yerusalemu, adzalanga mfumu ya Asuri chifukwa cha mwano umene uli mumtima mwake ndiponso chifukwa chakuti amayangʼana monyada ndi modzikuza.+
18 Abusa ako ayamba kuodzera, iwe mfumu ya Asuri,Ndipo anthu ako olemekezeka akungokhala mʼnyumba zawo. Anthu ako amwazikana mʼmapiri,Ndipo palibe amene akuwasonkhanitsa.+
13 Iye adzaloza dzanja lake kumpoto ndipo adzawononga Asuri.Adzachititsa Nineve kukhala bwinja,+ kukhala dziko louma ngati chipululu.