Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 “Yehova adzautsa mtundu wakutali, kumalekezero a dziko,+ mtundu umene chilankhulo chake sudzachimva.+ Mtunduwo udzakuukira monga mmene chiwombankhanga chimakhwathulira nyama yake,+

  • Yeremiya 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pakuti Yehova wanena kuti,+ ‘Ndikuitana mafuko onse a maufumu a kumpoto. Ndipo aliyense wa iwo adzabwera ndi kukhazikitsa mpando wake wachifumu pazipata za Yerusalemu.+ Iwo adzaukira mpanda wake wonse ndi mizinda yonse ya Yuda.+

  • Yeremiya 4:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Nenani zimenezi anthu inu. Nenani zimenezi kwa anthu a mitundu ina. Lengezani zimene zidzagwera Yerusalemu.”

      “Alonda akubwera kuchokera kudziko lakutali+ ndipo adzalengeza uthenga wa zimene zidzagwera mizinda ya Yuda.

  • Yeremiya 25:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 ndikuitana mafuko onse akumpoto,”+ watero Yehova, “ndipo ndikuitananso Nebukadirezara mfumu ya Babulo, mtumiki wanga.+ Ndikuitana anthu amenewa kuti aukire dziko lino+ ndi anthu okhala mmenemo, komanso kuti aukire mitundu yonse yokuzungulirani.+ Ndidzakuwonongani inuyo ndi mitundu yonse yokuzungulirani, ndi kukusandutsani chinthu chodabwitsa chimene azidzachiimbira mluzu+ ndipo malo anu adzakhala mabwinja mpaka kalekale.+

  • Ezekieli 7:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Chotero ndidzabweretsa anthu oipa kwambiri a mitundu ina+ ndipo iwo adzalanda nyumba zawo.+ Ndidzathetsa kunyada kwa anthu amphamvu+ ndipo malo awo opatulika adzaipitsidwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena