Deuteronomo 28:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 mtundu wa nkhope yoopsa+ umene sudzaikira kumbuyo munthu wachikulire kapena kukondera mnyamata.+ Ezekieli 21:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndidzakudzudzulani mwamphamvu. Ndidzakupemererani moto wa mkwiyo wanga,+ ndipo ndidzakuperekani m’manja mwa anthu osaganiza bwino, akatswiri odziwa kuwononga.+ Habakuku 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ine ndikuutsa Akasidi,+ mtundu waukali ndi waphuma umene ukupita kumalo otakasuka a padziko lapansi kukatenga malo amene si awo.+
31 Ndidzakudzudzulani mwamphamvu. Ndidzakupemererani moto wa mkwiyo wanga,+ ndipo ndidzakuperekani m’manja mwa anthu osaganiza bwino, akatswiri odziwa kuwononga.+
6 Ine ndikuutsa Akasidi,+ mtundu waukali ndi waphuma umene ukupita kumalo otakasuka a padziko lapansi kukatenga malo amene si awo.+