Numeri 32:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Nebo,+ Baala-meoni,+ ndi Sibima. Mayina a mizindayi anawasintha, n’kuipatsa mayina ena atsopano. Yoswa 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kiriyataimu,+ Sibima,+ Zereti-sahara, malo amene anali m’phiri la kuchigwa,