Yobu 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Magulu a amtengatenga a ku Tema+ amaifunafuna,Asabeya+ apaulendo amaidikirira. Yeremiya 25:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndinamwetsanso Dedani,+ Tema,+ Buza, onse odulira ndevu zawo zam’mbali,+