Mateyu 24:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 “Ndani kwenikweni amene ali kapolo wokhulupirika ndi wanzeru+ amene mbuye wake anamuika kuti aziyang’anira antchito ake apakhomo, ndi kuwapatsa chakudya pa nthawi yoyenera?+ 1 Akorinto 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Komanso pamenepa, chofunika kwa woyang’anira+ ndicho kukhala wokhulupirika.+
45 “Ndani kwenikweni amene ali kapolo wokhulupirika ndi wanzeru+ amene mbuye wake anamuika kuti aziyang’anira antchito ake apakhomo, ndi kuwapatsa chakudya pa nthawi yoyenera?+