Ezekieli 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye adzakhala malo oyanikapo makoka+ pakati pa nyanja.’+ “‘Ine ndanena, anthu a mitundu ina adzalanda zinthu zake,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. Ezekieli 26:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wauza mzinda wa Turo kuti, ‘Kodi zilumba sizidzagwedezeka chifukwa cha phokoso la kuwonongedwa kwako, kubuula kwa anthu ovulazidwa koopsa, ndi kuphedwa kwa anthu ako ambiri?+
5 Iye adzakhala malo oyanikapo makoka+ pakati pa nyanja.’+ “‘Ine ndanena, anthu a mitundu ina adzalanda zinthu zake,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
15 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wauza mzinda wa Turo kuti, ‘Kodi zilumba sizidzagwedezeka chifukwa cha phokoso la kuwonongedwa kwako, kubuula kwa anthu ovulazidwa koopsa, ndi kuphedwa kwa anthu ako ambiri?+