4 Zimenezi zili choncho chifukwa cha kuchuluka kwa zochita zake zauhule+ ndi kukongola kwake kochititsa kaso. Iye ndi mkazi waluso lamatsenga ndipo amakopa mitundu ya anthu ndi zochita zake zauhule, amakopa mitundu ya anthu ndi zochita zake zamatsenga.+