Salimo 88:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuyambira pa unyamata wanga ndakhala ndikusautsika komanso kutsala pang’ono kufa.+Ndapirira kwambiri zinthu zoopsa zochokera kwa inu.+
15 Kuyambira pa unyamata wanga ndakhala ndikusautsika komanso kutsala pang’ono kufa.+Ndapirira kwambiri zinthu zoopsa zochokera kwa inu.+