Yeremiya 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova wanena kuti: “Pita, ukatenge botolo la mafuta ladothi kwa woumba mbiya+ ndipo ukaitane ena mwa atsogoleri a anthu ndi ena mwa akuluakulu a ansembe.
19 Yehova wanena kuti: “Pita, ukatenge botolo la mafuta ladothi kwa woumba mbiya+ ndipo ukaitane ena mwa atsogoleri a anthu ndi ena mwa akuluakulu a ansembe.