Yeremiya 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Nyamuka, pita kunyumba ya woumba mbiya,+ ndipo ndikakuuza mawu anga kumeneko.” Aroma 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kodi simudziwa kuti woumba mbiya+ ali ndi ufulu woumba chiwiya china cholemekezeka, china chonyozeka kuchokera pa dongo limodzi?+
21 Kodi simudziwa kuti woumba mbiya+ ali ndi ufulu woumba chiwiya china cholemekezeka, china chonyozeka kuchokera pa dongo limodzi?+