1 Mafumu 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano Zedekiya mwana wa Kenaana anayandikira Mikaya ndipo anam’menya mbama,+ n’kunena kuti: “Kodi mzimu wa Yehova wachoka bwanji kwa ine n’kukalankhula ndi iwe?”+
24 Tsopano Zedekiya mwana wa Kenaana anayandikira Mikaya ndipo anam’menya mbama,+ n’kunena kuti: “Kodi mzimu wa Yehova wachoka bwanji kwa ine n’kukalankhula ndi iwe?”+