Hoseya 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno Yehova anauza Hoseya kuti: “Mwanayu umupatse dzina lakuti Yezereeli,+ pakuti kwatsala kanthawi kochepa kuti ndiimbe Yezereeli* mlandu wokhetsa magazi, mlandu wa nyumba ya Yehu.+ Pamenepo ndidzathetsa ufumu wolamulira nyumba ya Isiraeli,+
4 Ndiyeno Yehova anauza Hoseya kuti: “Mwanayu umupatse dzina lakuti Yezereeli,+ pakuti kwatsala kanthawi kochepa kuti ndiimbe Yezereeli* mlandu wokhetsa magazi, mlandu wa nyumba ya Yehu.+ Pamenepo ndidzathetsa ufumu wolamulira nyumba ya Isiraeli,+