Salimo 47:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti Yehova, Wam’mwambamwamba, ndi wochititsa mantha,+Ndiye Mfumu yaikulu padziko lonse lapansi.+ Salimo 66:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Bwerani anthu inu, kuti muone ntchito za Mulungu.+Zimene wachitira ana a anthu ndi zochititsa mantha.+
2 Pakuti Yehova, Wam’mwambamwamba, ndi wochititsa mantha,+Ndiye Mfumu yaikulu padziko lonse lapansi.+
5 Bwerani anthu inu, kuti muone ntchito za Mulungu.+Zimene wachitira ana a anthu ndi zochititsa mantha.+