Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Pamenepo iye adzati, ‘Ili kuti milungu yawo,+

      Thanthwe limene anathawirako,+

  • Oweruza 10:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma inu munandisiya+ n’kuyamba kutumikira milungu ina.+ N’chifukwa chake sindidzakupulumutsaninso.+

  • Yesaya 45:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “Sonkhanani pamodzi n’kubwera kwa ine.+ Unjikanani pamodzi, inu anthu opulumuka ku mitundu ya anthu.+ Amene amanyamula chifaniziro chawo chosema chamtengo sadziwa kanthu, mofanana ndi amene amapemphera kwa mulungu woti sangawapulumutse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena