Oweruza 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pitani, kapempheni thandizo kwa milungu+ imene mwasankhayo.+ Milungu imeneyo ndi imene ikupulumutseni pa nthawi ya nsautso yanu.” Yeremiya 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Kodi milungu yako imene wadzipangira ili kuti?+ Imeneyo ibwere kwa iwe ngati ingathe kukupulumutsa pa nthawi ya tsoka.+ Pakuti iwe Yuda, milungu yako yachuluka mofanana ndi mizinda yako.+
14 Pitani, kapempheni thandizo kwa milungu+ imene mwasankhayo.+ Milungu imeneyo ndi imene ikupulumutseni pa nthawi ya nsautso yanu.”
28 “Kodi milungu yako imene wadzipangira ili kuti?+ Imeneyo ibwere kwa iwe ngati ingathe kukupulumutsa pa nthawi ya tsoka.+ Pakuti iwe Yuda, milungu yako yachuluka mofanana ndi mizinda yako.+