Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Pamenepo iye adzati, ‘Ili kuti milungu yawo,+

      Thanthwe limene anathawirako,+

  • 1 Mafumu 18:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Pofika masana Eliya anayamba kuwaseka+ ndipo anali kunena kuti: “Muitaneni mokuwa kwambiri chifukwa iye ndi mulungu.+ Mwina watanganidwa ndi zinazake, kapena wapita kuchimbudzi.+ Mwinanso wagona, ndipo muyenera kum’dzutsa.”+

  • Yeremiya 2:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 “Kodi milungu yako imene wadzipangira ili kuti?+ Imeneyo ibwere kwa iwe ngati ingathe kukupulumutsa pa nthawi ya tsoka.+ Pakuti iwe Yuda, milungu yako yachuluka mofanana ndi mizinda yako.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena