Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 24:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Patapita nthawi, Sauli anafika kumakola a nkhosa amiyala m’mphepete mwa msewu, kumene kunali phanga. Choncho Sauli analowa mmenemo kukadzithandiza.+ Davide ndi amuna amene anali kuyenda naye anali atakhala pansi m’zigawo za mkatikati za phangalo,+ kumbuyo kwambiri.

  • Oweruza 3:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 iyeyo n’kutuluka panja.+

      Pamenepo atumiki a Egiloni anafika n’kuyamba kuyang’ana, ndipo anapeza zitseko za chipinda cha padenga zili zokhoma. Ndiyeno anati: “Ayenera kuti akudzithandiza+ m’chipinda chozizira bwino cha mkatikati.”

  • Mateyu 15:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Inunso simudziwa kodi kuti chilichonse cholowa m’kamwa chimadutsa m’matumbo ndipo chimakatayidwa kuchimbudzi?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena