Deuteronomo 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Uzikhalanso ndi chokumbira pamodzi ndi zida zako. Ndiyeno podzithandiza kunja kwa msasa, uzikumba dzenje ndi chokumbiracho ndipo ukamaliza kudzithandiza uzitembenuka ndi kufotsera zoipazo.+ Oweruza 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 iyeyo n’kutuluka panja.+ Pamenepo atumiki a Egiloni anafika n’kuyamba kuyang’ana, ndipo anapeza zitseko za chipinda cha padenga zili zokhoma. Ndiyeno anati: “Ayenera kuti akudzithandiza+ m’chipinda chozizira bwino cha mkatikati.” 1 Mafumu 18:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pofika masana Eliya anayamba kuwaseka+ ndipo anali kunena kuti: “Muitaneni mokuwa kwambiri chifukwa iye ndi mulungu.+ Mwina watanganidwa ndi zinazake, kapena wapita kuchimbudzi.+ Mwinanso wagona, ndipo muyenera kum’dzutsa.”+
13 Uzikhalanso ndi chokumbira pamodzi ndi zida zako. Ndiyeno podzithandiza kunja kwa msasa, uzikumba dzenje ndi chokumbiracho ndipo ukamaliza kudzithandiza uzitembenuka ndi kufotsera zoipazo.+
24 iyeyo n’kutuluka panja.+ Pamenepo atumiki a Egiloni anafika n’kuyamba kuyang’ana, ndipo anapeza zitseko za chipinda cha padenga zili zokhoma. Ndiyeno anati: “Ayenera kuti akudzithandiza+ m’chipinda chozizira bwino cha mkatikati.”
27 Pofika masana Eliya anayamba kuwaseka+ ndipo anali kunena kuti: “Muitaneni mokuwa kwambiri chifukwa iye ndi mulungu.+ Mwina watanganidwa ndi zinazake, kapena wapita kuchimbudzi.+ Mwinanso wagona, ndipo muyenera kum’dzutsa.”+