Mlaliki 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ngati nkhwangwa yabuntha ndipo munthu sanainole,+ adzawononga mphamvu zake pachabe. Choncho kugwiritsa ntchito bwino nzeru kumapindulitsa.+
10 Ngati nkhwangwa yabuntha ndipo munthu sanainole,+ adzawononga mphamvu zake pachabe. Choncho kugwiritsa ntchito bwino nzeru kumapindulitsa.+