-
Deuteronomo 23:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Pa zida zanu pazikhalanso chokumbira. Ndiyeno mukafuna kudzithandiza kunja kwa msasa, muzikumba dzenje ndi chokumbiracho ndipo mukamaliza muzikwirira zoipazo.
-