Deuteronomo 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Uzikhalanso ndi chokumbira pamodzi ndi zida zako. Ndiyeno podzithandiza kunja kwa msasa, uzikumba dzenje ndi chokumbiracho ndipo ukamaliza kudzithandiza uzitembenuka ndi kufotsera zoipazo.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:13 Nsanja ya Olonda,6/1/2012, tsa. 6 Chinsinsi cha Banja, ptsa. 46-47 Galamukani!,12/8/1991, tsa. 22
13 Uzikhalanso ndi chokumbira pamodzi ndi zida zako. Ndiyeno podzithandiza kunja kwa msasa, uzikumba dzenje ndi chokumbiracho ndipo ukamaliza kudzithandiza uzitembenuka ndi kufotsera zoipazo.+
23:13 Nsanja ya Olonda,6/1/2012, tsa. 6 Chinsinsi cha Banja, ptsa. 46-47 Galamukani!,12/8/1991, tsa. 22